Baibulo ya ana

Nthano zokondedwa mu Baibulo. Zaulele.

Cholinga chathu

Mateyu 19:14 Yesu anati, 'Muwasiye ana abwere kwa ine, musawaletse, pakuti ufumu waku mwamba ndiwa totele.

Baibulo la ana alipo kuti ana amudziwe Yesu Khristu kupyolera muku gawa nthano zambaibulo zojambulidwa, ndi zina zotero mosiyana siyana, kuphatikizapo Wide Web, lamya yammanja/PDA's, zolembedwa pama pepala akalala, mabuku akalala, muchiyankhulidwe chomwe mwana angayankhule.

Mabaibulo awa ndiwo gawila ana 1.8 bilioni apaziko lonse mwaulele momwe zingathekele.

Mutha kusayina kuti azikutumilani makalata